Ban on Sale of Petrol in Containers
With immediate effect, the Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) has banned the buying of Petrol in jerrycans or drums from any Fuel Service Station across the country until further notice. This decision has been arrived at to complement the efforts of fuel importers to restore the security of fuel supply in the shortest period.
Any Fuel Service Station found, or reported to be selling Petrol in jerrycans will have its operating licence suspended immediately.
Please report any illegal fuel trading practices to MERA on 09 9255 8564 or 08 8886 5686 or email: mera@mera.mw .
CHILETSO CHOGULITSA PETULO MU ZIGUBU
Bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) likudziwitsa eni a ma Fuel Service Station (Filling Station) ndi ma kasitomala awo kuti kuyambira lero, pa 20 November 2024 laletsa kugulitsa Petulo mu zigubu kapena mu ma diramu m’dziko lino. Chiletsochi chakhazikitsidwa kuti ntchito yobwezeretsanso mafuta okwanira m’dziko muno ichitike mwamsanga.
Filling Station iliyonse imene ipezeke ikunyozera chiletsochi idzatsekedwa ndikulandidwa layisensi yochitira malonda amafuta.
Chonde dziwitsani MERA pamene Filling Station ya phwanya malamulo kapena ndondomeko za ntchito za mafuta. Mutha kuimbira 01 1177 4607 kapena 09 9255 8564 or 08 8886 5686 kapena tumizani email: mera@mera.mw .